-
Yeremiya 49:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Matenti awo, nkhosa zawo, nsalu za matenti awo
Ndi katundu wawo yense zidzatengedwa.
Ngamila zawo zidzalandidwa,
Ndipo anthu adzawalirira kuti, ‘Zochititsa mantha zili paliponse!’”
-