Yeremiya 49:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mahema awo,+ nkhosa zawo,+ nsalu za mahema awo ndi zinthu zawo zonse zidzatengedwa.+ Ngamila zawo+ zidzalandidwa. Anthu adzawalirira kuti, ‘Zochititsa mantha zili paliponse!’”+
29 Mahema awo,+ nkhosa zawo,+ nsalu za mahema awo ndi zinthu zawo zonse zidzatengedwa.+ Ngamila zawo+ zidzalandidwa. Anthu adzawalirira kuti, ‘Zochititsa mantha zili paliponse!’”+