-
Maliro 5:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Anyamata akunyamula mphero, ndipo tianyamata tikudzandira chifukwa cholemedwa ndi mitolo ya nkhuni.