Maliro 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anyamata awanyamulitsa mphero,+ ndipo tianyamata tadzandira polemedwa ndi mitolo ya nkhuni.+