Ezekieli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Utengeponso tsitsi lina nʼkuliponya pamoto kuti lipse. Pamotowo, padzabuka moto umene udzafalikire kunyumba yonse ya Isiraeli.+
4 Utengeponso tsitsi lina nʼkuliponya pamoto kuti lipse. Pamotowo, padzabuka moto umene udzafalikire kunyumba yonse ya Isiraeli.+