Ezekieli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Utengeponso tsitsi lina n’kuliponya pamoto kuti linyeke. Kuchokera pamoto umenewu, padzabuka moto umene udzafalikire kunyumba yonse ya Isiraeli.+
4 Utengeponso tsitsi lina n’kuliponya pamoto kuti linyeke. Kuchokera pamoto umenewu, padzabuka moto umene udzafalikire kunyumba yonse ya Isiraeli.+