-
Ezekieli 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Uyu ndi Yerusalemu. Ndamuika pakati pa anthu a mitundu ina ndipo wazunguliridwa ndi mayiko ena.
-