-
Ezekieli 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Uyu ndi Yerusalemu. Ndamuika pakati pa mitundu ya anthu ndipo wazunguliridwa ndi mayiko ena.
-