-
Ezekieli 10:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Pamene munthuyo anapita pakati pawo, akerubiwo anali ataima mbali yakumanja kwa nyumba yopatulika ndipo mtambo unadzaza bwalo lonse lamkati.
-