Ezekieli 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akerubiwo anali ataimirira mbali ya kumanja kwa nyumbayo pamene munthuyo anapita pakati pawo, ndipo mtambo unali utadzaza bwalo lonse lamkati.+
3 Akerubiwo anali ataimirira mbali ya kumanja kwa nyumbayo pamene munthuyo anapita pakati pawo, ndipo mtambo unali utadzaza bwalo lonse lamkati.+