Ezekieli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mʼmatupi onse a akerubiwo, kumsana kwawo, mʼmanja mwawo, mʼmapiko awo ndiponso mʼmawilo a akerubi onse 4 munali maso paliponse.+
12 Mʼmatupi onse a akerubiwo, kumsana kwawo, mʼmanja mwawo, mʼmapiko awo ndiponso mʼmawilo a akerubi onse 4 munali maso paliponse.+