Ezekieli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zamoyozo zinali ndi maso paliponse. Zinali ndi maso pamatupi awo, kumbuyo kwawo, m’manja awo, m’mapiko awo, ndiponso kuzungulira mawilo onse.+ Pambali pa kerubi aliyense mwa akerubi anayi amenewo, panali wilo.
12 Zamoyozo zinali ndi maso paliponse. Zinali ndi maso pamatupi awo, kumbuyo kwawo, m’manja awo, m’mapiko awo, ndiponso kuzungulira mawilo onse.+ Pambali pa kerubi aliyense mwa akerubi anayi amenewo, panali wilo.