-
Ezekieli 16:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Palibe amene anakumvera chisoni kuti akuchitire chilichonse mwa zinthu zimenezi. Palibe amene anakuchitira chifundo. Mʼmalomwake anakutaya patchire chifukwa anthu anadana nawe pa tsiku limene unabadwa.
-