Ezekieli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe diso limene linakumvera chisoni kuti likuchitire chimodzi mwa zinthu zimenezi chifukwa chochita nawe chifundo.+ Koma tsiku limene unabadwa, unaponyedwa pansi chifukwa anthu ananyansidwa nawe.
5 Palibe diso limene linakumvera chisoni kuti likuchitire chimodzi mwa zinthu zimenezi chifukwa chochita nawe chifundo.+ Koma tsiku limene unabadwa, unaponyedwa pansi chifukwa anthu ananyansidwa nawe.