Ezekieli 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako ndinakuveka chovala cha nsalu yopeta ndi nsapato za chikopa chabwino kwambiri.* Ndinakukulunga munsalu zabwino kwambiri nʼkukuveka zovala zamtengo wapatali.
10 Kenako ndinakuveka chovala cha nsalu yopeta ndi nsapato za chikopa chabwino kwambiri.* Ndinakukulunga munsalu zabwino kwambiri nʼkukuveka zovala zamtengo wapatali.