Ezekieli 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako ndinakuveka chovala cha nsalu yopeta+ ndi nsapato za chikopa cha katumbu.*+ Ndinakukulunga munsalu zabwino kwambiri+ n’kukufunditsa nsalu zamtengo wapatali.
10 Kenako ndinakuveka chovala cha nsalu yopeta+ ndi nsapato za chikopa cha katumbu.*+ Ndinakukulunga munsalu zabwino kwambiri+ n’kukufunditsa nsalu zamtengo wapatali.