Ezekieli 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Unatchuka* kwambiri pakati pa mitundu ya anthu+ chifukwa cha kukongola kwako. Zili choncho chifukwa kukongola kwako kunali kogometsa popeza ndinaika ulemerero wanga pa iwe,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
14 Unatchuka* kwambiri pakati pa mitundu ya anthu+ chifukwa cha kukongola kwako. Zili choncho chifukwa kukongola kwako kunali kogometsa popeza ndinaika ulemerero wanga pa iwe,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.