Ezekieli 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Dzina lako linatchuka pakati pa mitundu ya anthu chifukwa cha kukongola kwako, pakuti linali labwino kwambiri chifukwa cha ulemerero wanga umene ndinaika pa iwe,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
14 “‘Dzina lako linatchuka pakati pa mitundu ya anthu chifukwa cha kukongola kwako, pakuti linali labwino kwambiri chifukwa cha ulemerero wanga umene ndinaika pa iwe,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”