Ezekieli 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mtima wako unali wofooka kwambiri pamene unkachita zinthu zonsezi.* Wakhala ukuchita zinthu ngati hule lopanda manyazi!’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
30 Mtima wako unali wofooka kwambiri pamene unkachita zinthu zonsezi.* Wakhala ukuchita zinthu ngati hule lopanda manyazi!’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+