Ezekieli 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano iweyo wandikwiyitsa koopsa+ chifukwa cha zonse zimene wakhala ukuchitazi. Wakhala ukuchita ntchito za hule+ lopanda m’manyazi omwe,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
30 Tsopano iweyo wandikwiyitsa koopsa+ chifukwa cha zonse zimene wakhala ukuchitazi. Wakhala ukuchita ntchito za hule+ lopanda m’manyazi omwe,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.