-
Ezekieli 16:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 ‘Koma pamene unamanga malo oti uzilambirirapo milungu yabodza, pamalo oonekera bwino kwambiri mumsewu uliwonse komanso kukonza malo okwera mʼbwalo lililonse la mzinda, sunali ngati hule chifukwa unkakana kulipidwa.
-