-
Ezekieli 16:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 ‘Ngakhale kuti unaunjika mulu wako wadothi pamphambano m’misewu, komanso unapanga malo okwera m’bwalo lililonse la mzinda, unakhala wosiyana ndi hule chifukwa sunkafuna kulipidwa.
-