-
Ezekieli 16:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Iweyo umachita zosiyana ndi akazi ena amene amachita uhule. Palibe amene amachita uhule ngati mmene iwe umachitira. Iweyo ndi amene umapereka malipiro kwa amuna koma iwowo sakulipira. Zimene umachita nʼzosiyana ndi zimene mahule ena amachita.’
-