-
Ezekieli 16:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Iweyo umachita zosiyana ndi akazi ena pa uhule wako, ndipo palibenso amene amachita uhule wofanana ndi wako, womapereka malipiro pamene iweyo sunalipidwe. Choncho iwe ukuchita zosiyana ndi anzako.’
-