Ezekieli 16:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 zoipa zako zisanaonekere.+ Koma pano ana aakazi a Siriya ndi anthu oyandikana naye akukunyoza komanso ana aakazi a Afilisiti+ ndi onse amene akuzungulira akukuchitira zachipongwe.
57 zoipa zako zisanaonekere.+ Koma pano ana aakazi a Siriya ndi anthu oyandikana naye akukunyoza komanso ana aakazi a Afilisiti+ ndi onse amene akuzungulira akukuchitira zachipongwe.