Ezekieli 16:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Zoipa zako zisanaonekere,+ Sodomu sanali woti n’kumveka ukumutchula ngati mmene zinalili pa nthawi imene ana aakazi a Siriya+ ndi onse omuzungulira, komanso ana aakazi a Afilisiti,+ anali kukunyoza kuchokera kumbali zonse.+
57 Zoipa zako zisanaonekere,+ Sodomu sanali woti n’kumveka ukumutchula ngati mmene zinalili pa nthawi imene ana aakazi a Siriya+ ndi onse omuzungulira, komanso ana aakazi a Afilisiti,+ anali kukunyoza kuchokera kumbali zonse.+