-
Ezekieli 19:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mkango waukazi uja unadikira koma patapita nthawi unaona kuti palibe chiyembekezo chakuti mwanayo adzabwereranso.
Choncho unatenga mwana wake wina nʼkumutumiza ngati mkango wamphamvu.
-