Ezekieli 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Mkango waukazi uja utaona kuti wadikira popanda chilichonse chochitika, ndipo palibenso chiyembekezo chilichonse, unatenganso mwana wake wina.+ Unalera mwanayo mpaka kukhala mkango wamphamvu.
5 “‘Mkango waukazi uja utaona kuti wadikira popanda chilichonse chochitika, ndipo palibenso chiyembekezo chilichonse, unatenganso mwana wake wina.+ Unalera mwanayo mpaka kukhala mkango wamphamvu.