Ezekieli 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzapereka Mowabu limodzi ndi Aamoni kwa anthu a Kumʼmawa+ kuti akhale chuma chawo. Ndidzachita zimenezi kuti Aamoni asadzakumbukiridwenso pakati pa mitundu ya anthu.+
10 Ndidzapereka Mowabu limodzi ndi Aamoni kwa anthu a Kumʼmawa+ kuti akhale chuma chawo. Ndidzachita zimenezi kuti Aamoni asadzakumbukiridwenso pakati pa mitundu ya anthu.+