Ezekieli 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mitengo imeneyi yatsikira ku Manda* pamodzi ndi mtengo wa mkungudzawo. Yatsikira kwa ophedwa ndi lupanga+ limodzi ndi amene ankamuthandiza* omwe ankakhala mumthunzi wake pakati pa mitundu ina ya anthu.’+
17 Mitengo imeneyi yatsikira ku Manda* pamodzi ndi mtengo wa mkungudzawo. Yatsikira kwa ophedwa ndi lupanga+ limodzi ndi amene ankamuthandiza* omwe ankakhala mumthunzi wake pakati pa mitundu ina ya anthu.’+