Ezekieli 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati pa nyumbazo* panali njira+ imene inali mikono 10 mulifupi ndi mikono 100 mulitali* ndipo makomo olowera mʼnyumbazo anali mbali yakumpoto.
4 Pakati pa nyumbazo* panali njira+ imene inali mikono 10 mulifupi ndi mikono 100 mulitali* ndipo makomo olowera mʼnyumbazo anali mbali yakumpoto.