-
Ezekieli 48:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Kumbali yakumʼmwera mzindawo ukhale mikono 4,500 ndipo kukhale mageti atatu awa: Geti limodzi likhale ndi dzina lakuti Simiyoni, geti lina Isakara ndipo lina Zebuloni.
-