-
Ezekieli 48:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 “Malire a mzindawo a mbali ya kum’mwera akhale mikono 4,500. Kumeneko kukhalenso zipata zitatu. Kukhale chipata chimodzi chotchedwa Simiyoni, chipata chimodzi chotchedwa Isakara, ndi chipata chimodzi chotchedwa Zebuloni.
-