Danieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo. Anthu amenewa anafika nʼkuima pamaso pa mfumu.+
2 Choncho mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo. Anthu amenewa anafika nʼkuima pamaso pa mfumu.+