Danieli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno usiku, chinsinsicho chinaululidwa kwa Danieli mʼmasomphenya.+ Choncho Danieli anatamanda Mulungu wakumwamba.
19 Ndiyeno usiku, chinsinsicho chinaululidwa kwa Danieli mʼmasomphenya.+ Choncho Danieli anatamanda Mulungu wakumwamba.