Danieli 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 inuyo amene Mulungu wakupatsani mphamvu zolamulira anthu kulikonse kumene akukhala komanso nyama zakutchire ndi mbalame zamumlengalenga, amene Mulungu wakuikani kuti muzilamulira zonsezi,+ inuyo ndi mutu wagolide.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:38 Ulosi wa Danieli, tsa. 50 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 5
38 inuyo amene Mulungu wakupatsani mphamvu zolamulira anthu kulikonse kumene akukhala komanso nyama zakutchire ndi mbalame zamumlengalenga, amene Mulungu wakuikani kuti muzilamulira zonsezi,+ inuyo ndi mutu wagolide.+