Danieli 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ufumu wa nambala 4 udzakhala wolimba ngati chitsulo.+ Mofanana ndi chitsulo chimene chimaphwanya nʼkupera china chilichonse, ufumuwo udzaphwanya nʼkuwonongeratu maufumu ena onsewa.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:40 Ulosi wa Danieli, ptsa. 55-57 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, ptsa. 5-6
40 Ufumu wa nambala 4 udzakhala wolimba ngati chitsulo.+ Mofanana ndi chitsulo chimene chimaphwanya nʼkupera china chilichonse, ufumuwo udzaphwanya nʼkuwonongeratu maufumu ena onsewa.+