Danieli 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo zilombo 4 zikuluzikulu+ zinatuluka mʼnyanjayo. Chilombo chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Ulosi wa Danieli, tsa. 130 Nsanja ya Olonda,10/1/1986, tsa. 7
3 Ndipo zilombo 4 zikuluzikulu+ zinatuluka mʼnyanjayo. Chilombo chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake.