Danieli 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zilombo zinayi zikuluzikulu+ zinali kutuluka m’nyanjayo,+ ndipo chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Ulosi wa Danieli, tsa. 130 Nsanja ya Olonda,10/1/1986, tsa. 7
3 Zilombo zinayi zikuluzikulu+ zinali kutuluka m’nyanjayo,+ ndipo chilichonse chinali chosiyana ndi chinzake.+