Danieli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinayandikira mmodzi mwa amene anali ataimirira kuti ndimufunse tanthauzo la zonsezi.+ Choncho iye anandifotokozera kumasulira kwa nkhani zimenezi, kuti:
16 Ndinayandikira mmodzi mwa amene anali ataimirira kuti ndimufunse tanthauzo la zonsezi.+ Choncho iye anandifotokozera kumasulira kwa nkhani zimenezi, kuti: