Danieli 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10. Pambuyo pa mafumu amenewa padzatulukanso mfumu ina imene idzakhale yosiyana ndi oyambawa ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:24 Ulosi wa Danieli, ptsa. 135-141 Mawu a Mulungu, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, ptsa. 24-25
24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10. Pambuyo pa mafumu amenewa padzatulukanso mfumu ina imene idzakhale yosiyana ndi oyambawa ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+
7:24 Ulosi wa Danieli, ptsa. 135-141 Mawu a Mulungu, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, ptsa. 24-25