Danieli 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:24 Ulosi wa Danieli, ptsa. 135-141 Mawu a Mulungu, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, ptsa. 24-25
24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+
7:24 Ulosi wa Danieli, ptsa. 135-141 Mawu a Mulungu, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, ptsa. 24-25