Danieli 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Bwalo la milandu linayamba kuzenga mlandu ndipo linachotsa ulamuliro wa mfumuyo nʼcholinga choti mfumuyo aiwonongeretu.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:26 Ulosi wa Danieli, tsa. 145
26 Koma Bwalo la milandu linayamba kuzenga mlandu ndipo linachotsa ulamuliro wa mfumuyo nʼcholinga choti mfumuyo aiwonongeretu.+