Danieli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyamba aja.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Ulosi wa Danieli, tsa. 165
8 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyamba aja.+