Danieli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼchaka choyamba cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara+ ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Ndiyeno analemba zimene analotazo+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo. Danieli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ineyo Danieli, ndinavutika kwambiri mumtima chifukwa masomphenya amene ndinaona ankandichititsa mantha.+
7 Mʼchaka choyamba cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara+ ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Ndiyeno analemba zimene analotazo+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo.
15 Koma ineyo Danieli, ndinavutika kwambiri mumtima chifukwa masomphenya amene ndinaona ankandichititsa mantha.+