Danieli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ndinayangʼana kwa Yehova Mulungu woona ndipo ndinapemphera momuchonderera, ndinasala kudya,+ ndinavala ziguduli komanso kudzithira phulusa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:3 Ulosi wa Danieli, tsa. 182
3 Choncho ndinayangʼana kwa Yehova Mulungu woona ndipo ndinapemphera momuchonderera, ndinasala kudya,+ ndinavala ziguduli komanso kudzithira phulusa.