Danieli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu mwachitadi zimene munachenjeza kuti mudzachitira ifeyo+ ndi atsogoleri athu amene ankatilamulira.* Mwachita zimenezi potigwetsera tsoka lalikulu. Zimene zachitika mu Yerusalemu sizinayambe zachitikapo padziko lonse lapansi.+
12 Inu mwachitadi zimene munachenjeza kuti mudzachitira ifeyo+ ndi atsogoleri athu amene ankatilamulira.* Mwachita zimenezi potigwetsera tsoka lalikulu. Zimene zachitika mu Yerusalemu sizinayambe zachitikapo padziko lonse lapansi.+