Danieli 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose, masoka onsewa atigwera.+ Koma sitinapemphe inu Yehova Mulungu wathu kuti mutikomere mtima.* Sitinachite zimenezi posiya zolakwa zathu+ komanso posonyeza kuti tikumvetsa choonadi chanu.* Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:13 Ulosi wa Danieli, tsa. 183
13 Mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose, masoka onsewa atigwera.+ Koma sitinapemphe inu Yehova Mulungu wathu kuti mutikomere mtima.* Sitinachite zimenezi posiya zolakwa zathu+ komanso posonyeza kuti tikumvetsa choonadi chanu.*