-
Danieli 11:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 chifukwa sitima zapamadzi za ku Kitimu+ zidzabwera kudzamuukira ndipo adzachititsidwa manyazi.
Iye adzabwerera kwawo ndipo adzalankhula mawu amphamvu odzudzula* pangano lopatulika+ moti adzakwaniritsa zolinga zake. Adzabwerera kwawo ndithu ndipo adzayamba kuganizira za anthu amene akusiya pangano lopatulika.
-