30 Choncho zombo za ku Kitimu+ zidzabwera ndi kumuukira ndipo adzakhala wachisoni.
“Iye adzabwerera ndi kulankhula mawu amphamvu odzudzula+ pangano lopatulika+ ndipo adzachita zofuna zake. Pamenepo iye adzabwerera ndi kuganizira anthu osiya pangano lopatulika.